Miyambo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwana wanga, tamvera malangizo a bambo ako,+ ndipo usasiye malamulo a mayi ako,+ Miyambo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gwira malangizo,+ usawataye.+ Uwasunge bwino chifukwa iwo ndiwo moyo wako.+ Miyambo 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Landirani malangizo* anga osati siliva, ndiponso kudziwa zinthu m’malo mwa golide wabwino kwambiri.+ Zefaniya 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno ndinati, ‘Mosakayikira udzandiopa ndipo udzalola kulangizidwa’+ kuti malo ake okhala asawonongedwe,+ pakuti ndidzamuimba mlandu wa zonsezi.+ Koma zinthu zawo zonse zimene anali kuchita zinali zowawonongetsa ndipo anazichitadi mofulumira.+ Aheberi 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kupirira kumene mukupiriraku,+ mukupirira kuti chikhale chilango chanu. Mulungu akuchita nanu zinthu ngati ana ake.+ Ndi mwana wanji amene bambo ake samulanga?+
10 Landirani malangizo* anga osati siliva, ndiponso kudziwa zinthu m’malo mwa golide wabwino kwambiri.+
7 Ndiyeno ndinati, ‘Mosakayikira udzandiopa ndipo udzalola kulangizidwa’+ kuti malo ake okhala asawonongedwe,+ pakuti ndidzamuimba mlandu wa zonsezi.+ Koma zinthu zawo zonse zimene anali kuchita zinali zowawonongetsa ndipo anazichitadi mofulumira.+
7 Kupirira kumene mukupiriraku,+ mukupirira kuti chikhale chilango chanu. Mulungu akuchita nanu zinthu ngati ana ake.+ Ndi mwana wanji amene bambo ake samulanga?+