Yesaya 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 N’chiyaninso chimene ndingachite m’munda wanga wa mpesawu chimene sindinachitemo kale?+ Ine ndinali kuyembekezera kuti ubereka mphesa zabwino, koma n’chifukwa chiyani unabereka mphesa zam’tchire? Yesaya 63:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anati: “Ndithu awa ndi anthu anga,+ ana amene sadzachita zachinyengo.”+ Choncho iye anakhala Mpulumutsi wawo.+ Luka 19:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Iye anati: “Iwe ukanazindikira+ lero zinthu zamtendere . . . koma tsopano zabisika kuti usathe kuziona.+ 2 Petulo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova sakuchedwa kukwaniritsa lonjezo lake,+ ngati mmene anthu ena amaonera kuti akuchedwa, koma akuleza nanu mtima, pakuti safuna kuti wina aliyense adzawonongedwe, koma amafuna kuti anthu onse alape.+
4 N’chiyaninso chimene ndingachite m’munda wanga wa mpesawu chimene sindinachitemo kale?+ Ine ndinali kuyembekezera kuti ubereka mphesa zabwino, koma n’chifukwa chiyani unabereka mphesa zam’tchire?
8 Iye anati: “Ndithu awa ndi anthu anga,+ ana amene sadzachita zachinyengo.”+ Choncho iye anakhala Mpulumutsi wawo.+
42 Iye anati: “Iwe ukanazindikira+ lero zinthu zamtendere . . . koma tsopano zabisika kuti usathe kuziona.+
9 Yehova sakuchedwa kukwaniritsa lonjezo lake,+ ngati mmene anthu ena amaonera kuti akuchedwa, koma akuleza nanu mtima, pakuti safuna kuti wina aliyense adzawonongedwe, koma amafuna kuti anthu onse alape.+