13 “‘Unachita zonyansa chifukwa cha khalidwe lako lotayirira.+ Ine ndinayesetsa kukuyeretsa, koma zonyansa zako sizinachoke.+ Sudzayeranso kufikira nditathetsera mkwiyo wanga pa iwe.+
51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+