Ekisodo 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho pa tsiku limenelo Yehova anapulumutsa Isiraeli m’manja mwa Aiguputo,+ ndipo Isiraeli anaona Aiguputo atafa m’mphepete mwa nyanja.+ Salimo 106:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo anaiwala Mulungu, Mpulumutsi wawo,+Amene anachita zinthu zazikulu ku Iguputo,+
30 Choncho pa tsiku limenelo Yehova anapulumutsa Isiraeli m’manja mwa Aiguputo,+ ndipo Isiraeli anaona Aiguputo atafa m’mphepete mwa nyanja.+