Salimo 58:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wolungama adzasangalala chifukwa chakuti waona oipa akupatsidwa chilango.+Adzasambitsa mapazi ake m’magazi a anthu oipa.+ Salimo 59:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mulungu amene wandisonyeza kukoma mtima kosatha ndidzaonana naye maso ndi maso.+Mulungu adzachititsa kuti ndione adani anga, adaniwo atagonja.+ Salimo 91:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Udzayang’ana ndi maso ako,+Ndipo udzaona anthu oipa akulandira chilango.+ Miyambo 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova anapanga chilichonse n’cholinga,+ ndipo ngakhale woipa anamusungira tsiku loipa.+
10 Wolungama adzasangalala chifukwa chakuti waona oipa akupatsidwa chilango.+Adzasambitsa mapazi ake m’magazi a anthu oipa.+
10 Mulungu amene wandisonyeza kukoma mtima kosatha ndidzaonana naye maso ndi maso.+Mulungu adzachititsa kuti ndione adani anga, adaniwo atagonja.+