Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 ndi kuwakhomereza mwa ana ako.+ Uzilankhula nawo za mawuwo ukakhala pansi m’nyumba mwako, poyenda pamsewu, pogona+ ndi podzuka.

  • Miyambo 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ananu, mverani malangizo* a bambo anu.+ Mvetserani kuti mupeze luso lomvetsa zinthu.+

  • Miyambo 6:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Mwana wanga, sunga lamulo la bambo ako,+ ndipo usasiye malangizo a mayi ako.+

  • Aefeso 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Inunso abambo, musamapsetse mtima ana anu,+ koma muwalere+ m’malangizo*+ a Yehova* ndi kuwaphunzitsa kaganizidwe+ kake.

  • Aheberi 12:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiponso, bambo athu otibereka, amene anali ndi thupi lanyama ngati lathuli anali kutilanga,+ ndipo tinali kuwalemekeza. Kuli bwanji ndi Atate wa moyo wathu wauzimu. Kodi sitiyenera kuwagonjera koposa pamenepo kuti tikhale ndi moyo?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena