Deuteronomo 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Munthu akakhala ndi mwana wamwamuna wosamvera ndi wopanduka,+ amene samvera mawu a bambo ake kapena a mayi ake,+ ndipo amulangiza koma sawamvera,+ Aefeso 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ananu, muzimvera makolo anu+ mwa+ Ambuye, pakuti kuchita zimenezi n’chilungamo.+
18 “Munthu akakhala ndi mwana wamwamuna wosamvera ndi wopanduka,+ amene samvera mawu a bambo ake kapena a mayi ake,+ ndipo amulangiza koma sawamvera,+