Miyambo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwana wanga, usakane malangizo* a Yehova+ ndipo usanyansidwe ndi kudzudzula kwake,+ Miyambo 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu wosakwapula mwana wake ndiye kuti akumuda,+ koma womukonda ndi amene amamuyang’anira kuti amulangize.+ Miyambo 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Langa mwana wako padakali chiyembekezo,+ ndipo usalakelake imfa yake.+ 2 Timoteyo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Malemba onse anauziridwa ndi Mulungu,+ ndipo ndi opindulitsa pa kuphunzitsa,+ kudzudzula,+ kuwongola zinthu+ ndi kulangiza m’chilungamo,+
24 Munthu wosakwapula mwana wake ndiye kuti akumuda,+ koma womukonda ndi amene amamuyang’anira kuti amulangize.+
16 Malemba onse anauziridwa ndi Mulungu,+ ndipo ndi opindulitsa pa kuphunzitsa,+ kudzudzula,+ kuwongola zinthu+ ndi kulangiza m’chilungamo,+