Miyambo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 chifukwa Yehova amadzudzula munthu amene amam’konda,+ monga momwe bambo amadzudzulira mwana amene amakondwera naye.+ Yohane 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo iye akadzafika adzapereka umboni wotsimikizika ku dzikoli wonena za tchimo, za chilungamo, ndi za chiweruzo.+ Tito 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 wogwira mwamphamvu mawu okhulupirika pamene akuphunzitsa mwaluso,+ kuti athe kulimbikitsa anthu ndi chiphunzitso cholondola+ ndiponso kudzudzula+ otsutsa.
12 chifukwa Yehova amadzudzula munthu amene amam’konda,+ monga momwe bambo amadzudzulira mwana amene amakondwera naye.+
8 Ndipo iye akadzafika adzapereka umboni wotsimikizika ku dzikoli wonena za tchimo, za chilungamo, ndi za chiweruzo.+
9 wogwira mwamphamvu mawu okhulupirika pamene akuphunzitsa mwaluso,+ kuti athe kulimbikitsa anthu ndi chiphunzitso cholondola+ ndiponso kudzudzula+ otsutsa.