1 Akorinto 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Komabe tikaweruzidwa,+ ndiye kuti taphunzitsidwa ndi Yehova+ kuti tisalandire chilango+ pamodzi ndi dziko.+ Aheberi 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+ Chivumbulutso 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Onse amene ndimawakonda, ndimawadzudzula ndi kuwalanga.+ Choncho, khala wodzipereka ndipo ulape.+
32 Komabe tikaweruzidwa,+ ndiye kuti taphunzitsidwa ndi Yehova+ kuti tisalandire chilango+ pamodzi ndi dziko.+
6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+
19 “‘Onse amene ndimawakonda, ndimawadzudzula ndi kuwalanga.+ Choncho, khala wodzipereka ndipo ulape.+