Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 ndi kuwakhomereza mwa ana ako.+ Uzilankhula nawo za mawuwo ukakhala pansi m’nyumba mwako, poyenda pamsewu, pogona+ ndi podzuka.

  • Miyambo 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 chifukwa Yehova amadzudzula munthu amene amam’konda,+ monga momwe bambo amadzudzulira mwana amene amakondwera naye.+

  • Miyambo 19:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Langa mwana wako padakali chiyembekezo,+ ndipo usalakelake imfa yake.+

  • Miyambo 22:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Uchitsiru umakhazikika mumtima mwa mwana.+ Koma ndodo yomulangira* ndi imene imauthamangitsira kutali ndi iye.+

  • Miyambo 23:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Um’kwapule ndi chikwapu, kuti upulumutse moyo wake ku Manda.+

  • Aefeso 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Inunso abambo, musamapsetse mtima ana anu,+ koma muwalere+ m’malangizo*+ a Yehova* ndi kuwaphunzitsa kaganizidwe+ kake.

  • Aheberi 12:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena