Genesis 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero, Mulungu poyang’ana dziko lapansi anaona kuti laipa,+ chifukwa njira za anthu onse zinali zitaipa.+ Deuteronomo 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo achita okha zinthu zowawonongetsa,+Si ana ake, chilemacho n’chawo.+Iwo ndiwo m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota!+ Hoseya 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aisiraeli azama nazo zinthu zowononga+ ngati m’masiku a Gibeya.+ Mulungu adzakumbukira zolakwa zawo+ ndipo adzawalanga chifukwa cha machimo awo. Mika 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Tsoka kwa anthu amene amati akagona pabedi, amakonza chiwembu ndiponso kuganiza mmene angachitire zoipa.+ M’mawa kukangocha, iwo amazichitadi+ chifukwa chakuti ali ndi mphamvu zochitira zimenezo.+
12 Chotero, Mulungu poyang’ana dziko lapansi anaona kuti laipa,+ chifukwa njira za anthu onse zinali zitaipa.+
5 Iwo achita okha zinthu zowawonongetsa,+Si ana ake, chilemacho n’chawo.+Iwo ndiwo m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota!+
9 Aisiraeli azama nazo zinthu zowononga+ ngati m’masiku a Gibeya.+ Mulungu adzakumbukira zolakwa zawo+ ndipo adzawalanga chifukwa cha machimo awo.
2 “Tsoka kwa anthu amene amati akagona pabedi, amakonza chiwembu ndiponso kuganiza mmene angachitire zoipa.+ M’mawa kukangocha, iwo amazichitadi+ chifukwa chakuti ali ndi mphamvu zochitira zimenezo.+