Genesis 31:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndikanatha kukuchitani choipa anthu inu,+ koma Mulungu wa bambo anu analankhula nane usiku wapitawu kuti, ‘Samala kuti usanene chilichonse chosokoneza zochita za Yakobo.’+ 1 Mafumu 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yezebeli mkazi wake anamuuza kuti: “Kodi muziwalamulira chonchi Aisiraeliwa?+ Dzukani, idyani chakudya, mtima wanu usangalale. Ineyo ndikupatsani munda wa mpesa wa Naboti Myezereeli.”+ Yohane 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Pilato anati: “Kodi sukundilankhula?+ Kodi sukudziwa kuti ine ndili ndi mphamvu yokumasula, komanso yokupachika?”
29 Ndikanatha kukuchitani choipa anthu inu,+ koma Mulungu wa bambo anu analankhula nane usiku wapitawu kuti, ‘Samala kuti usanene chilichonse chosokoneza zochita za Yakobo.’+
7 Ndiyeno Yezebeli mkazi wake anamuuza kuti: “Kodi muziwalamulira chonchi Aisiraeliwa?+ Dzukani, idyani chakudya, mtima wanu usangalale. Ineyo ndikupatsani munda wa mpesa wa Naboti Myezereeli.”+
10 Pamenepo Pilato anati: “Kodi sukundilankhula?+ Kodi sukudziwa kuti ine ndili ndi mphamvu yokumasula, komanso yokupachika?”