Genesis 31:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma bambo anu akhala akundipusitsa, ndipo asintha malipiro anga maulendo 10. Ngakhale ndi choncho, Mulungu sanawalole kuti andichite choipa.+ Genesis 31:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma usiku m’maloto,+ Mulungu anafikira Labani Msiriyayo+ n’kumuuza kuti: “Samala kuti usanene chilichonse chosokoneza zochita za Yakobo.”+ Machitidwe 5:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma ngati ikuchokera kwa Mulungu,+ simungathe kuwaletsa.+ Mukaumirira mukhoza kupezeka kuti mukulimbana ndi Mulungu.”+
7 Koma bambo anu akhala akundipusitsa, ndipo asintha malipiro anga maulendo 10. Ngakhale ndi choncho, Mulungu sanawalole kuti andichite choipa.+
24 Koma usiku m’maloto,+ Mulungu anafikira Labani Msiriyayo+ n’kumuuza kuti: “Samala kuti usanene chilichonse chosokoneza zochita za Yakobo.”+
39 Koma ngati ikuchokera kwa Mulungu,+ simungathe kuwaletsa.+ Mukaumirira mukhoza kupezeka kuti mukulimbana ndi Mulungu.”+