Genesis 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Isaki anali ndi zaka 40 pamene anakwatira Rabeka, mwana wa Betuele,+ Msiriya+ wa ku Padana-ramu, mlongo wake wa Labani, Msiriya. Deuteronomo 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo uzikanena pamaso pa Yehova Mulungu wako kuti, ‘Bambo anga anali Msiriya+ wotsala pang’ono kufa. Anapita ku Iguputo+ ndi anthu ochepa chabe+ a m’banja lake kukakhala kumeneko monga mlendo, koma anakhaladi mtundu waukulu ndi wamphamvu kumeneko.+ Hoseya 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yakobo anathawira kumunda wa ku Siriya+ ndipo Isiraeli+ anapitirizabe kugwira ntchito+ ndi kulondera nkhosa kuti apeze mkazi.+
20 Isaki anali ndi zaka 40 pamene anakwatira Rabeka, mwana wa Betuele,+ Msiriya+ wa ku Padana-ramu, mlongo wake wa Labani, Msiriya.
5 Pamenepo uzikanena pamaso pa Yehova Mulungu wako kuti, ‘Bambo anga anali Msiriya+ wotsala pang’ono kufa. Anapita ku Iguputo+ ndi anthu ochepa chabe+ a m’banja lake kukakhala kumeneko monga mlendo, koma anakhaladi mtundu waukulu ndi wamphamvu kumeneko.+
12 Yakobo anathawira kumunda wa ku Siriya+ ndipo Isiraeli+ anapitirizabe kugwira ntchito+ ndi kulondera nkhosa kuti apeze mkazi.+