Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 28:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Chotero Isaki anatumiza Yakobo, ndipo iye ananyamuka ulendo wopita ku Padana-ramu. Anapita kwa Labani mwana wa Betuele, Msiriya.+ Labaniyo anali mlongo wake wa Rabeka,+ mayi ake a Yakobo ndi Esau.+

  • Genesis 31:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Zonse pamodzi ndakhala zaka 20 m’nyumba mwanu. Ndakugwirirani ntchito zaka 14, kugwirira ana anu aakazi awiriwa. Zaka zinanso 6, ndagwirira ntchito ziweto. Koma inu munapitiriza kusinthasintha malipiro anga mpaka maulendo 10.+

  • Genesis 31:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Mulungu wa bambo anga,+ Mulungu wa Abulahamu, Mulungu amene Isaki anali kumuopa,+ akanapanda kukhala kumbali yanga, bwenzi mutandibweza kwathu chimanjamanja. Koma Mulungu waona kusautsika kwanga ndi ntchito zimene ndagwira molimbika, n’chifukwa chake anakudzudzulani usiku wapitawu.”+

  • Hoseya 12:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Yakobo anathawira kumunda wa ku Siriya+ ndipo Isiraeli+ anapitirizabe kugwira ntchito+ ndi kulondera nkhosa kuti apeze mkazi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena