Genesis 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamwamba pa makwererowo anaonapo Yehova, amene anamuuza kuti:+ “Ine ndine Yehova, Mulungu wa Abulahamu kholo lako, ndi Mulungu wa Isaki.+ Dziko limene wagonapoli ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+ Genesis 31:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndikanatha kukuchitani choipa anthu inu,+ koma Mulungu wa bambo anu analankhula nane usiku wapitawu kuti, ‘Samala kuti usanene chilichonse chosokoneza zochita za Yakobo.’+
13 Pamwamba pa makwererowo anaonapo Yehova, amene anamuuza kuti:+ “Ine ndine Yehova, Mulungu wa Abulahamu kholo lako, ndi Mulungu wa Isaki.+ Dziko limene wagonapoli ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+
29 Ndikanatha kukuchitani choipa anthu inu,+ koma Mulungu wa bambo anu analankhula nane usiku wapitawu kuti, ‘Samala kuti usanene chilichonse chosokoneza zochita za Yakobo.’+