Salimo 52:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 N’chifukwa chiyani ukudzitukumula chifukwa cha zinthu zoipa, wamphamvu iwe?+Kukoma mtima kosatha kwa Mulungu n’kokhalitsa.+ Yohane 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Pilato anati: “Kodi sukundilankhula?+ Kodi sukudziwa kuti ine ndili ndi mphamvu yokumasula, komanso yokupachika?”
52 N’chifukwa chiyani ukudzitukumula chifukwa cha zinthu zoipa, wamphamvu iwe?+Kukoma mtima kosatha kwa Mulungu n’kokhalitsa.+
10 Pamenepo Pilato anati: “Kodi sukundilankhula?+ Kodi sukudziwa kuti ine ndili ndi mphamvu yokumasula, komanso yokupachika?”