Genesis 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kusi anabereka Nimurodi,+ amene anali woyamba kukhala wamphamvu padziko lapansi. 1 Samueli 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano tsiku limenelo, mmodzi wa atumiki a Sauli, dzina lake Doegi,+ Mwedomu,+ anali kumeneko chifukwa anali atamusunga+ pamaso pa Yehova. Iye anali mkulu wa abusa a Sauli.+ Salimo 94:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo amalankhula zopanda pake, ndipo amalankhula mosasamala.+Onse ochita zopweteka anzawo amadzitukumula.+
7 Tsopano tsiku limenelo, mmodzi wa atumiki a Sauli, dzina lake Doegi,+ Mwedomu,+ anali kumeneko chifukwa anali atamusunga+ pamaso pa Yehova. Iye anali mkulu wa abusa a Sauli.+
4 Iwo amalankhula zopanda pake, ndipo amalankhula mosasamala.+Onse ochita zopweteka anzawo amadzitukumula.+