Salimo 31:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Milomo yachinyengo isowe chonena,+Milomo imene ikulankhula motsutsana ndi wolungama,+ yosadziletsa pa kudzikweza ndi kunyoza ena.+ Salimo 73:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kudzikweza kwawo kwafika kumwamba,+Akuyendayenda padziko lapansi ndipo lilime lawo likunena zilizonse zimene akufuna.+ Salimo 144:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Odala ndi anthu amene zimenezi zikuwachitikira.”Ayi, koma odala ndi anthu amene Mulungu wawo ndi Yehova.+
18 Milomo yachinyengo isowe chonena,+Milomo imene ikulankhula motsutsana ndi wolungama,+ yosadziletsa pa kudzikweza ndi kunyoza ena.+
9 Kudzikweza kwawo kwafika kumwamba,+Akuyendayenda padziko lapansi ndipo lilime lawo likunena zilizonse zimene akufuna.+
15 Odala ndi anthu amene zimenezi zikuwachitikira.”Ayi, koma odala ndi anthu amene Mulungu wawo ndi Yehova.+