2 Mbiri 32:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atumiki a Senakeribuwo analankhula zinthu zinanso zonyoza Yehova Mulungu woona+ ndi Hezekiya mtumiki wake. Mateyu 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Wophunzira amangofanana ndi mphunzitsi wake, ndipo kapolo amangofanana ndi mbuye wake.+ Ngati anthu atchula mwininyumba kuti Belezebule,*+ kuli bwanji ena a m’banja lakelo, kodi sadzawanena zoposa pamenepa? Machitidwe 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Paulo atafika, Ayuda amene anabwera kuchokera ku Yerusalemu, anaima momuzungulira n’kumamuneneza milandu yoopsa yambiri,+ imene sanathe kupereka umboni wake.
16 Atumiki a Senakeribuwo analankhula zinthu zinanso zonyoza Yehova Mulungu woona+ ndi Hezekiya mtumiki wake.
25 Wophunzira amangofanana ndi mphunzitsi wake, ndipo kapolo amangofanana ndi mbuye wake.+ Ngati anthu atchula mwininyumba kuti Belezebule,*+ kuli bwanji ena a m’banja lakelo, kodi sadzawanena zoposa pamenepa?
7 Paulo atafika, Ayuda amene anabwera kuchokera ku Yerusalemu, anaima momuzungulira n’kumamuneneza milandu yoopsa yambiri,+ imene sanathe kupereka umboni wake.