Mateyu 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndinu odala pamene anthu akukunyozani+ ndi kukuzunzani,+ komanso kukunamizirani zoipa zilizonse chifukwa cha ine. Luka 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno anayamba kumuneneza+ kuti: “Ife tapeza munthu uyu akupandutsa+ mtundu wathu ndi kuletsa anthu kuti asamakhome msonkho+ kwa Kaisara, komanso iyeyu akunena kuti ndi Khristu mfumu.”+ Machitidwe 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ife tapeza kuti munthu uyu ndi wovutitsa kwabasi,+ ndipo akuyambitsa zoukira boma+ pakati pa Ayuda onse padziko lapansi kumene kuli anthu. Ndiponso ndi mtsogoleri wa gulu lampatuko wa Anazareti.+
11 “Ndinu odala pamene anthu akukunyozani+ ndi kukuzunzani,+ komanso kukunamizirani zoipa zilizonse chifukwa cha ine.
2 Ndiyeno anayamba kumuneneza+ kuti: “Ife tapeza munthu uyu akupandutsa+ mtundu wathu ndi kuletsa anthu kuti asamakhome msonkho+ kwa Kaisara, komanso iyeyu akunena kuti ndi Khristu mfumu.”+
5 Ife tapeza kuti munthu uyu ndi wovutitsa kwabasi,+ ndipo akuyambitsa zoukira boma+ pakati pa Ayuda onse padziko lapansi kumene kuli anthu. Ndiponso ndi mtsogoleri wa gulu lampatuko wa Anazareti.+