Mateyu 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Afarisi atamva zimenezi ananena kuti: “Ameneyutu sikuti amatulutsa ziwanda ndi mphamvu zake ayi. Amatero ndi mphamvu ya Belezebule, wolamulira ziwanda.”+ Maliko 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komanso alembi amene anachokera ku Yerusalemu anali kunena kuti: “Ali ndi Belezebule,* ndipo amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya wolamulira ziwanda.”+ Luka 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ena mwa iwo anati: “Ameneyu amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebule* wolamulira wa ziwanda.”+ Yohane 8:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Poyankha Ayudawo anati: “Kodi tikamanena kuti, Ndiwe Msamariya+ ndipo uli ndi chiwanda,+ tikulakwitsa ngati?”
24 Afarisi atamva zimenezi ananena kuti: “Ameneyutu sikuti amatulutsa ziwanda ndi mphamvu zake ayi. Amatero ndi mphamvu ya Belezebule, wolamulira ziwanda.”+
22 Komanso alembi amene anachokera ku Yerusalemu anali kunena kuti: “Ali ndi Belezebule,* ndipo amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya wolamulira ziwanda.”+
15 Koma ena mwa iwo anati: “Ameneyu amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebule* wolamulira wa ziwanda.”+
48 Poyankha Ayudawo anati: “Kodi tikamanena kuti, Ndiwe Msamariya+ ndipo uli ndi chiwanda,+ tikulakwitsa ngati?”