Luka 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ena mwa iwo ananena kuti: “Ameneyu amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebule,* wolamulira ziwanda.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:15 Yesu—Ndi Njira, tsa. 176
15 Koma ena mwa iwo ananena kuti: “Ameneyu amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebule,* wolamulira ziwanda.”+