Maliko 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komanso alembi amene anachokera ku Yerusalemu anali kunena kuti: “Ali ndi Belezebule,* ndipo amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya wolamulira ziwanda.”+ Luka 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ena mwa iwo anati: “Ameneyu amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebule* wolamulira wa ziwanda.”+
22 Komanso alembi amene anachokera ku Yerusalemu anali kunena kuti: “Ali ndi Belezebule,* ndipo amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya wolamulira ziwanda.”+
15 Koma ena mwa iwo anati: “Ameneyu amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebule* wolamulira wa ziwanda.”+