Mateyu 9:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma Afarisi anayamba kunena kuti: “Ameneyu amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya wolamulira ziwanda.”+ Mateyu 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Wophunzira amangofanana ndi mphunzitsi wake, ndipo kapolo amangofanana ndi mbuye wake.+ Ngati anthu atchula mwininyumba kuti Belezebule,*+ kuli bwanji ena a m’banja lakelo, kodi sadzawanena zoposa pamenepa? Luka 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ena mwa iwo anati: “Ameneyu amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebule* wolamulira wa ziwanda.”+ Yohane 8:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Poyankha Ayudawo anati: “Kodi tikamanena kuti, Ndiwe Msamariya+ ndipo uli ndi chiwanda,+ tikulakwitsa ngati?”
34 Koma Afarisi anayamba kunena kuti: “Ameneyu amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya wolamulira ziwanda.”+
25 Wophunzira amangofanana ndi mphunzitsi wake, ndipo kapolo amangofanana ndi mbuye wake.+ Ngati anthu atchula mwininyumba kuti Belezebule,*+ kuli bwanji ena a m’banja lakelo, kodi sadzawanena zoposa pamenepa?
15 Koma ena mwa iwo anati: “Ameneyu amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebule* wolamulira wa ziwanda.”+
48 Poyankha Ayudawo anati: “Kodi tikamanena kuti, Ndiwe Msamariya+ ndipo uli ndi chiwanda,+ tikulakwitsa ngati?”