Mateyu 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Wophunzira amangofanana ndi mphunzitsi wake ndipo kapolo amangofanana ndi mbuye wake.+ Ngati anthu atchula mwininyumba kuti Belezebule,*+ kuli bwanji ena a mʼbanja lakelo?
25 Wophunzira amangofanana ndi mphunzitsi wake ndipo kapolo amangofanana ndi mbuye wake.+ Ngati anthu atchula mwininyumba kuti Belezebule,*+ kuli bwanji ena a mʼbanja lakelo?