Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 12:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Afarisi atamva zimenezi ananena kuti: “Ameneyutu sikuti amatulutsa ziwanda ndi mphamvu zake ayi koma ndi mphamvu za Belezebule,* wolamulira ziwanda.”+

  • Maliko 3:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Komanso alembi amene anachokera ku Yerusalemu ankanena kuti: “Ali ndi Belezebule,* ndipo amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya wolamulira ziwanda.”+

  • Luka 11:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma ena mwa iwo ananena kuti: “Ameneyu amatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebule,* wolamulira ziwanda.”+

  • Yohane 8:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Ayudawo anamuyankha kuti: “Kodi tikunama tikamanena kuti, ‘Ndiwe Msamariya+ ndipo uli ndi chiwandaʼ?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena