Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 12:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Afarisi atamva zimenezi ananena kuti: “Ameneyutu sikuti amatulutsa ziwanda ndi mphamvu zake ayi koma ndi mphamvu za Belezebule,* wolamulira ziwanda.”+

  • Yohane 7:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Gulu la anthulo linayankha kuti: “Uli ndi chiwanda iwe. Akufuna kukupha ndi ndani?”

  • Yohane 10:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ambiri a iwo ankanena kuti: “Ameneyu ali ndi chiwanda ndipo ndi wamisala. Nʼchifukwa chiyani mukumumvetsera?”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena