9 Pamenepo Doegi,+ Mwedomu, amene anali mkulu wa atumiki a Sauli anayankha kuti: “Ineyo ndinaona mwana wa Jese atabwera ku Nobu kwa Ahimeleki,+ mwana wa Ahitubu.+
Kwa wotsogolera nyimbo. Masikili.* Salimo la Davide, pa nthawi imene Doegi, Mwedomu, anapita kwa Sauli kukamuuza kuti Davide wapita kunyumba ya Ahimeleki.+