7 Tsopano tsiku limenelo, mmodzi wa atumiki a Sauli, dzina lake Doegi,+ Mwedomu,+ anali kumeneko chifukwa anali atamusunga+ pamaso pa Yehova. Iye anali mkulu wa abusa a Sauli.+
Kwa wotsogolera nyimbo. Masikili.* Salimo la Davide, pa nthawi imene Doegi, Mwedomu, anapita kwa Sauli kukamuuza kuti Davide wapita kunyumba ya Ahimeleki.+