Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pa zoweta zanu+ idzatengapo gawo limodzi mwa magawo 10, ndipo inuyo mudzakhala antchito ake.

  • 1 Samueli 11:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno Sauli anatulukira kuchokera kutchire, akuyenda pambuyo pa ziweto. Kenako anati: “Kodi chachitika n’chiyani kuti anthuwa azilira?” Motero anayamba kum’fotokozera mawu a amuna a ku Yabesi.

  • 1 Mbiri 27:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Sitirai wa ku Sharoni+ anali kuyang’anira zoweta zimene anali kudyetsera ku Sharoni. Safati mwana wa Adilai anali kuyang’anira zoweta zimene zinali kuzigwa.

  • 2 Mbiri 26:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iye anamanganso nsanja+ m’chipululu ndipo anakumba zitsime zambiri (popeza anakhala ndi ziweto zambiri). Anapanganso zomwezo ku Sefela+ ndi kudera lokwererapo. Kumapiri ndi ku Karimeli kunali alimi ndi anthu osamalira minda ya mpesa popeza iye ankakonda ulimi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena