Genesis 31:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma usiku m’maloto,+ Mulungu anafikira Labani Msiriyayo+ n’kumuuza kuti: “Samala kuti usanene chilichonse chosokoneza zochita za Yakobo.”+ Salimo 31:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndidzakondwera ndi kusangalala chifukwa cha kukoma mtima kwanu kosatha,+Pakuti mwaona kusautsika kwanga.+Mwadziwa zowawa zimene zandigwera,+
24 Koma usiku m’maloto,+ Mulungu anafikira Labani Msiriyayo+ n’kumuuza kuti: “Samala kuti usanene chilichonse chosokoneza zochita za Yakobo.”+
7 Ndidzakondwera ndi kusangalala chifukwa cha kukoma mtima kwanu kosatha,+Pakuti mwaona kusautsika kwanga.+Mwadziwa zowawa zimene zandigwera,+