Salimo 142:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinachita zimenezi pamene mtima wanga+ unalefuka.Pamenepo, munadziwa njira yanga.+Adani anga anditchera msampha+M’njira imene ndikuyenda.+ 1 Akorinto 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ngati munthu akukonda Mulungu,+ ameneyo amadziwika kwa Mulungu.+ Agalatiya 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma tsopano pamene mwadziwa Mulungu, kapena tinene kuti tsopano pamene mwadziwidwa ndi Mulungu,+ mukubwereranso bwanji ku mfundo zachibwanabwana,+ zomwe ndi zosathandiza ndiponso zopanda pake,+ n’kumafuna kukhalanso akapolo ake?+
3 Ndinachita zimenezi pamene mtima wanga+ unalefuka.Pamenepo, munadziwa njira yanga.+Adani anga anditchera msampha+M’njira imene ndikuyenda.+
9 Koma tsopano pamene mwadziwa Mulungu, kapena tinene kuti tsopano pamene mwadziwidwa ndi Mulungu,+ mukubwereranso bwanji ku mfundo zachibwanabwana,+ zomwe ndi zosathandiza ndiponso zopanda pake,+ n’kumafuna kukhalanso akapolo ake?+