Akolose 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngati munafa+ limodzi ndi Khristu pa mfundo zimene ndi maziko+ a moyo wa m’dzikoli,+ n’chifukwa chiyani mukupitiriza kukhala ngati kuti mudakali mbali ya dzikoli, pogonjeranso malamulo+ akuti:
20 Ngati munafa+ limodzi ndi Khristu pa mfundo zimene ndi maziko+ a moyo wa m’dzikoli,+ n’chifukwa chiyani mukupitiriza kukhala ngati kuti mudakali mbali ya dzikoli, pogonjeranso malamulo+ akuti: