Akolose 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngati munafa limodzi ndi Khristu ndipo simukutsatiranso mfundo zimene anthu amʼdzikoli amayendera,+ nʼchifukwa chiyani mukupitiriza kukhala ngati mudakali mbali ya dzikoli, pogonjeranso malamulo akuti:+
20 Ngati munafa limodzi ndi Khristu ndipo simukutsatiranso mfundo zimene anthu amʼdzikoli amayendera,+ nʼchifukwa chiyani mukupitiriza kukhala ngati mudakali mbali ya dzikoli, pogonjeranso malamulo akuti:+