1 Akorinto 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ngati munthu akukonda Mulungu,+ ameneyo amadziwika kwa Mulungu.+