Ekisodo 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Mose anauza Yehova kuti: “Inu mukundiuza kuti, ‘Tsogolera anthuwa,’ koma simunandidziwitse amene mudzam’tuma kuti ndiyende naye limodzi. Komanso mwanena kuti ‘Ndikukudziwa bwino, ndi dzina lako lomwe,+ ndipo ndakukomera mtima.’ Nahumu 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova ndi wabwino+ ndipo ndi malo achitetezo+ pa tsiku la nsautso.+ Amadziwa amene amathawira kwa iye kuti apeze chitetezo.+
12 Tsopano Mose anauza Yehova kuti: “Inu mukundiuza kuti, ‘Tsogolera anthuwa,’ koma simunandidziwitse amene mudzam’tuma kuti ndiyende naye limodzi. Komanso mwanena kuti ‘Ndikukudziwa bwino, ndi dzina lako lomwe,+ ndipo ndakukomera mtima.’
7 Yehova ndi wabwino+ ndipo ndi malo achitetezo+ pa tsiku la nsautso.+ Amadziwa amene amathawira kwa iye kuti apeze chitetezo.+