Aroma 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu anatsutsa uchimo mwa kugwiritsa ntchito thupi potumiza Mwana wake+ m’thupi lofanana ndi lauchimo+ kuti athane ndi uchimo.+ Pakuti Chilamulo sichinathe kuchita zimenezi+ pokhala chofooka+ chifukwa cha thupi. Aheberi 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithudi, ndiye kuti malamulo oyambawo akuchotsedwa chifukwa chakuti ndi ofooka+ ndiponso operewera.+
3 Mulungu anatsutsa uchimo mwa kugwiritsa ntchito thupi potumiza Mwana wake+ m’thupi lofanana ndi lauchimo+ kuti athane ndi uchimo.+ Pakuti Chilamulo sichinathe kuchita zimenezi+ pokhala chofooka+ chifukwa cha thupi.
18 Ndithudi, ndiye kuti malamulo oyambawo akuchotsedwa chifukwa chakuti ndi ofooka+ ndiponso operewera.+