Genesis 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pambuyo pake Mulungu anafikira Abimeleki usiku m’maloto n’kumuuza kuti: “Ufatu iwe chifukwa cha mkazi amene watengayu,+ pakuti ndi mkazi wa mwini.”+ Mateyu 27:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komanso atakhala pampando woweruzira milandu, mkazi wake anamutumizira mawu akuti: “Nkhani ya munthu wolungamayu isakukhudzeni.+ Inetu ndavutika kwambiri lero m’maloto+ chifukwa cha iyeyu.”
3 Pambuyo pake Mulungu anafikira Abimeleki usiku m’maloto n’kumuuza kuti: “Ufatu iwe chifukwa cha mkazi amene watengayu,+ pakuti ndi mkazi wa mwini.”+
19 Komanso atakhala pampando woweruzira milandu, mkazi wake anamutumizira mawu akuti: “Nkhani ya munthu wolungamayu isakukhudzeni.+ Inetu ndavutika kwambiri lero m’maloto+ chifukwa cha iyeyu.”