Salimo 78:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo asadzakhale ngati makolo awo,+M’badwo wosamva ndi wopanduka,+M’badwo umene sunakonze mtima wawo,+Ndipo maganizo awo sanali okhulupirika kwa Mulungu.+ Luka 9:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Poyankha Yesu anati: “Inu a m’badwo+ wopanda chikhulupiriro ndi wopotoka maganizo, kodi ndikhala nanube ndi kupitiriza kukupirirani mpaka liti? Bwera naye kuno mwana wakoyo.”+ Afilipi 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezani nacho ndiponso osalakwa.+ Mukhale ana a Mulungu opanda chilema+ pakati pa m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota,+ umene mukuwala pakati pawo monga zounikira m’dzikoli.+
8 Ndipo asadzakhale ngati makolo awo,+M’badwo wosamva ndi wopanduka,+M’badwo umene sunakonze mtima wawo,+Ndipo maganizo awo sanali okhulupirika kwa Mulungu.+
41 Poyankha Yesu anati: “Inu a m’badwo+ wopanda chikhulupiriro ndi wopotoka maganizo, kodi ndikhala nanube ndi kupitiriza kukupirirani mpaka liti? Bwera naye kuno mwana wakoyo.”+
15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezani nacho ndiponso osalakwa.+ Mukhale ana a Mulungu opanda chilema+ pakati pa m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota,+ umene mukuwala pakati pawo monga zounikira m’dzikoli.+