Luka 9:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Yesu anayankha kuti: “Inu mʼbadwo wopanda chikhulupiriro ndi wopotoka maganizo,+ kodi ndikhala nanube mpaka liti? Ndipitirize kukupirirani mpaka liti? Bwera naye kuno mwana wakoyo.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:41 Yesu—Ndi Njira, tsa. 146 Nsanja ya Olonda,1/15/1988, tsa. 8
41 Yesu anayankha kuti: “Inu mʼbadwo wopanda chikhulupiriro ndi wopotoka maganizo,+ kodi ndikhala nanube mpaka liti? Ndipitirize kukupirirani mpaka liti? Bwera naye kuno mwana wakoyo.”+