2 Mbiri 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma iye anachita zoipa+ chifukwa sanatsimikize kufunafuna Yehova ndi mtima wake wonse.+ Salimo 81:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho ndinawasiya kuti apitirize kuumitsa mtima wawo.+Iwo anapitiriza kuyenda mu nzeru zawo.+ Yeremiya 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma anthu awa ali ndi mtima wouma ndi wopanduka. Achoka panjira yanga ndipo akuyenda m’njira yawo.+ Yeremiya 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma iwo sanamvere kapena kutchera khutu,+ ndipo anapitiriza kuyenda mwa zofuna zawo, mwa kuuma kwa mtima wawo woipawo,+ mwakuti anali kuyenda mobwerera m’mbuyo osati mopita patsogolo,+
23 Koma anthu awa ali ndi mtima wouma ndi wopanduka. Achoka panjira yanga ndipo akuyenda m’njira yawo.+
24 Koma iwo sanamvere kapena kutchera khutu,+ ndipo anapitiriza kuyenda mwa zofuna zawo, mwa kuuma kwa mtima wawo woipawo,+ mwakuti anali kuyenda mobwerera m’mbuyo osati mopita patsogolo,+