Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 5:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Zikanakhala bwino kwambiri akanakhala ndi mtima wondiopa+ ndi kusunga malamulo anga+ nthawi zonse, kuti iwo ndi ana awo zinthu ziwayendere bwino mpaka kalekale!*+

  • 1 Samueli 7:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Zitatero, Samueli anauza nyumba yonse ya Isiraeli kuti: “Ngati mukubwereradi kwa Yehova+ ndi mtima wanu wonse, chotsani milungu yachilendo pakati panu.+ Muchotsenso zifaniziro za Asitoreti,+ ndi kulunjikitsa mitima yanu kwa Yehova mosayang’ananso kwina,+ ndi kutumikira iye yekha. Mukatero, adzakupulumutsani m’manja mwa Afilisiti.”+

  • 1 Mafumu 18:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Kenako Eliya anayandikira anthu onsewo n’kunena kuti: “Kodi mukayikakayika* mpaka liti?+ Ngati Yehova ali Mulungu woona m’tsateni,+ koma ngati Baala ndiye Mulungu woona tsatirani ameneyo.” Koma anthuwo sanamuyankhe chilichonse.

  • Maliko 12:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse, moyo wako wonse, maganizo ako onse ndi mphamvu zako zonse.’+

  • Aroma 12:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Chikondi+ chanu chisakhale cha chiphamaso.+ Nyansidwani ndi choipa,+ gwiritsitsani chabwino.+

  • Yakobo 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Nanunso khalani oleza mtima.+ Limbitsani mitima yanu, chifukwa kukhalapo kwa Ambuye kwayandikira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena