1 Atesalonika 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Achite zimenezi mpaka atalimbitsa mitima yanu ndi kukupangitsani kukhala opanda cholakwa+ ndi oyera pamaso pa Mulungu wathu ndi Atate, pa nthawi ya kukhalapo*+ kwa Ambuye wathu Yesu, limodzi ndi oyera ake onse.+
13 Achite zimenezi mpaka atalimbitsa mitima yanu ndi kukupangitsani kukhala opanda cholakwa+ ndi oyera pamaso pa Mulungu wathu ndi Atate, pa nthawi ya kukhalapo*+ kwa Ambuye wathu Yesu, limodzi ndi oyera ake onse.+