Deuteronomo 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uziopa Yehova Mulungu wako+ ndi kum’tumikira,+ ndipo uzilumbira pa dzina lake.+ Deuteronomo 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Muziopa Yehova Mulungu wanu.+ Muzim’tumikira,+ kum’mamatira+ ndi kulumbira pa dzina lake.+ Deuteronomo 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Muzitsatira Yehova Mulungu wanu, muzimuopa, muzisunga malamulo ake, muzimvera mawu ake, muzim’tumikira ndi kum’mamatira.+ Luka 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Poyankha Yesu anamuuza kuti: “Malemba amati, ‘Yehova* Mulungu wako+ ndi amene uyenera kumulambira, ndipo uyenera kutumikira iye yekha basi.’”+
4 Muzitsatira Yehova Mulungu wanu, muzimuopa, muzisunga malamulo ake, muzimvera mawu ake, muzim’tumikira ndi kum’mamatira.+
8 Poyankha Yesu anamuuza kuti: “Malemba amati, ‘Yehova* Mulungu wako+ ndi amene uyenera kumulambira, ndipo uyenera kutumikira iye yekha basi.’”+