Aheberi 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pitirizani kuchita zimenezi kuti musakhale aulesi,+ koma mukhale otsanzira+ anthu amene, mwa chikhulupiriro ndi kuleza mtima, akulandira zinthu zimene Mulungu analonjeza monga cholowa chawo.+
12 Pitirizani kuchita zimenezi kuti musakhale aulesi,+ koma mukhale otsanzira+ anthu amene, mwa chikhulupiriro ndi kuleza mtima, akulandira zinthu zimene Mulungu analonjeza monga cholowa chawo.+