1 Mafumu 15:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ ndiponso anapitiriza kuyenda m’njira ya Yerobowamu+ ndi m’tchimo lake limene anachimwitsa nalo Isiraeli.+
34 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ ndiponso anapitiriza kuyenda m’njira ya Yerobowamu+ ndi m’tchimo lake limene anachimwitsa nalo Isiraeli.+