-
1 Mafumu 16:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mawu a Yehova otsutsana ndi Basa ndi nyumba yake+ anafikira Yehu mwana wa Haneni mneneri. Mawuwo anali otsutsana naye chifukwa cha zoipa zonse zimene Basayo anachita pamaso pa Yehova mwa kumukwiyitsa+ ndi ntchito ya manja ake,+ ndiponso chifukwa chakuti iye anapha+ Nadabu. Mawuwo anali akuti nyumba yake idzakhala ngati nyumba ya Yerobowamu.
-