Mateyu 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Poyankha Yesu anati: “Inu a m’badwo wopanda chikhulupiriro ndi wopotoka maganizo,+ kodi ndikhala nanube mpaka liti? Ndipitirize kukupirirani mpaka liti? Bwera nayeni kuno.” Maliko 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Poyankha iye anawauza kuti: “Inu a m’badwo wopanda chikhulupiriro,+ kodi ndikhala nanube mpaka liti? Ndipitirize kukupirirani mpaka liti? Bwera nayeni kuno.”+
17 Poyankha Yesu anati: “Inu a m’badwo wopanda chikhulupiriro ndi wopotoka maganizo,+ kodi ndikhala nanube mpaka liti? Ndipitirize kukupirirani mpaka liti? Bwera nayeni kuno.”
19 Poyankha iye anawauza kuti: “Inu a m’badwo wopanda chikhulupiriro,+ kodi ndikhala nanube mpaka liti? Ndipitirize kukupirirani mpaka liti? Bwera nayeni kuno.”+